Yesaya 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mulungu adzathetseratu ulemerero wa nkhalango yake ndi wa munda wake wa zipatso,Ndipo zidzakhala ngati munthu wodwala amene akuonda.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:18 Yesaya 1, ptsa. 149-150
18 Mulungu adzathetseratu ulemerero wa nkhalango yake ndi wa munda wake wa zipatso,Ndipo zidzakhala ngati munthu wodwala amene akuonda.+