-
Yesaya 10:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mitengo yotsala yamʼnkhalango mwake
Idzakhala yochepa kwambiri moti kamnyamata kadzatha kulemba chiwerengero chake.
-