Yesaya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku limenelo, otsala a IsiraeliNdi amʼnyumba ya Yakobo amene adzapulumukeSadzadaliranso amene anawamenya,+Koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova,Woyera wa Isiraeli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:20 Yesaya 1, ptsa. 155-156
20 Tsiku limenelo, otsala a IsiraeliNdi amʼnyumba ya Yakobo amene adzapulumukeSadzadaliranso amene anawamenya,+Koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova,Woyera wa Isiraeli.