Yesaya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale kuti anthu ako iwe Isiraeli,Ali ngati mchenga wakunyanja,Otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Mulungu wakonza zoti anthuwo awonongedwe+Ndipo chilango cholungama chidzawabwerera ngati madzi osefukira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:22 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 22 Yesaya 1, ptsa. 155-156
22 Ngakhale kuti anthu ako iwe Isiraeli,Ali ngati mchenga wakunyanja,Otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Mulungu wakonza zoti anthuwo awonongedwe+Ndipo chilango cholungama chidzawabwerera ngati madzi osefukira.+