Yesaya 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa pakangodutsa kanthawi kochepa, kudzudzulako kudzatha ndipo mkwiyo wanga udzawayakira, moti adzawonongedwa.+
25 Chifukwa pakangodutsa kanthawi kochepa, kudzudzulako kudzatha ndipo mkwiyo wanga udzawayakira, moti adzawonongedwa.+