Yesaya 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iwe mwana wamkazi wa Galimu, lira ndi kufuula kwambiri. Khala tcheru iwe Laisa, Iwenso Anatoti womvetsa chisoni!+
30 Iwe mwana wamkazi wa Galimu, lira ndi kufuula kwambiri. Khala tcheru iwe Laisa, Iwenso Anatoti womvetsa chisoni!+