Yesaya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+Mzimu wanzeru+ ndi womvetsa zinthu,Mzimu wopereka malangizo abwino ndi wamphamvu,+Mzimu wodziwa zinthu ndi woopa Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, ptsa. 16-1910/1/1992, ptsa. 18-197/1/1992, tsa. 14 Yesaya 1, ptsa. 159-160
2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+Mzimu wanzeru+ ndi womvetsa zinthu,Mzimu wopereka malangizo abwino ndi wamphamvu,+Mzimu wodziwa zinthu ndi woopa Yehova.
11:2 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, ptsa. 16-1910/1/1992, ptsa. 18-197/1/1992, tsa. 14 Yesaya 1, ptsa. 159-160