Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu nʼkusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumakona 4 a dziko lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:12 Galamukani!,12/2010, tsa. 28 Yesaya 1, ptsa. 166-167
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu nʼkusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumakona 4 a dziko lapansi.+