Yesaya 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzatsika zitunda za* Afilisiti kumadzulo.Onsewa pamodzi, adzalanda katundu wa anthu a Kumʼmawa. Adzatambasula dzanja lawo nʼkugonjetsa* Edomu+ ndi Mowabu,+Ndipo Aamoni adzawagonjera.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:14 Yesaya 1, ptsa. 167-168
14 Iwo adzatsika zitunda za* Afilisiti kumadzulo.Onsewa pamodzi, adzalanda katundu wa anthu a Kumʼmawa. Adzatambasula dzanja lawo nʼkugonjetsa* Edomu+ ndi Mowabu,+Ndipo Aamoni adzawagonjera.+