Yesaya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+Ngati mmene zinalili kwa Aisiraeli pamene ankatuluka mʼdziko la Iguputo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Yesaya 1, ptsa. 168-169
16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+Ngati mmene zinalili kwa Aisiraeli pamene ankatuluka mʼdziko la Iguputo.