Yesaya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja lanu,Kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:2 Yesaya 1, ptsa. 172-173
2 “Imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja lanu,Kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka.