Yesaya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndapereka lamulo kwa anthu amene ndawasankha.*+ Ndaitana asilikali anga kuti adzasonyeze mkwiyo wanga.Iwo amasangalala komanso kunyada. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Yesaya 1, ptsa. 173-174
3 Ine ndapereka lamulo kwa anthu amene ndawasankha.*+ Ndaitana asilikali anga kuti adzasonyeze mkwiyo wanga.Iwo amasangalala komanso kunyada.