Yesaya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:5 Yesaya 1, ptsa. 173-174
5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+