Yesaya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lirani mofuula, chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi. Lidzabwera ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:6 Yesaya 1, tsa. 174
6 Lirani mofuula, chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi. Lidzabwera ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.+