Yesaya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu apanikizika.+ Nsautso ndi zowawa zawagweraNgati mkazi amene akubereka. Akuyangʼanana mwamantha,Ndipo nkhope zawo zikuonekeratu kuti ali ndi nkhawa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:8 Yesaya 1, ptsa. 174-175
8 Anthu apanikizika.+ Nsautso ndi zowawa zawagweraNgati mkazi amene akubereka. Akuyangʼanana mwamantha,Ndipo nkhope zawo zikuonekeratu kuti ali ndi nkhawa.