Yesaya 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani! Tsiku la Yehova likubwera,Tsikulo ndi lankhanza, laukali ndiponso lamkwiyo woyaka moto,Likubwera kuti lidzachititse dziko kukhala chinthu chochititsa mantha,+Ndiponso kuti lidzawononge anthu ochimwa amʼdzikolo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:9 Yesaya 1, tsa. 175
9 Taonani! Tsiku la Yehova likubwera,Tsikulo ndi lankhanza, laukali ndiponso lamkwiyo woyaka moto,Likubwera kuti lidzachititse dziko kukhala chinthu chochititsa mantha,+Ndiponso kuti lidzawononge anthu ochimwa amʼdzikolo.