Yesaya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa nyenyezi zakumwamba ndi magulu awo*+Sizidzaonetsa kuwala kwawo.Dzuwa lidzachita mdima potuluka,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 109-110 Yesaya 1, tsa. 175
10 Chifukwa nyenyezi zakumwamba ndi magulu awo*+Sizidzaonetsa kuwala kwawo.Dzuwa lidzachita mdima potuluka,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.