Yesaya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzaimba mlandu anthu okhala padziko lapansi chifukwa cha zoipa zawo,+Ndiponso anthu oipa chifukwa cha zolakwa zawo. Ndidzathetsa kunyada kwa anthu odzikuzaNdidzatsitsa kudzikuza kwa olamulira ankhanza.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Yesaya 1, tsa. 175
11 Ndidzaimba mlandu anthu okhala padziko lapansi chifukwa cha zoipa zawo,+Ndiponso anthu oipa chifukwa cha zolakwa zawo. Ndidzathetsa kunyada kwa anthu odzikuzaNdidzatsitsa kudzikuza kwa olamulira ankhanza.+