Yesaya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndidzachititsa kuti kumwamba kunjenjemere,Ndipo dziko lapansi lidzagwedezeka nʼkuchoka mʼmalo mwake+Chifukwa cha ukali wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:13 Yesaya 1, tsa. 176
13 Choncho ndidzachititsa kuti kumwamba kunjenjemere,Ndipo dziko lapansi lidzagwedezeka nʼkuchoka mʼmalo mwake+Chifukwa cha ukali wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.