Yesaya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzachititsa kuti akhazikike* mʼdziko lawo,+ alendo adzagwirizana nawo ndipo adzakhala limodzi ndi nyumba ya Yakobo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Yesaya 1, ptsa. 181-182
14 Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzachititsa kuti akhazikike* mʼdziko lawo,+ alendo adzagwirizana nawo ndipo adzakhala limodzi ndi nyumba ya Yakobo.+