Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:4 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 30 Yesaya 1, ptsa. 182-183
4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+