Yesaya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale mitengo ya junipa* yasangalala ndi zimene zakuchitikira,Limodzi ndi mitengo ya mkungudza ya ku Lebanoni. Mitengoyi ikunena kuti, ‘Kuyambira pamene unaphedwa,Palibenso munthu wodula mitengo amene anabwera kudzatidula.’ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Yesaya 1, tsa. 183
8 Ngakhale mitengo ya junipa* yasangalala ndi zimene zakuchitikira,Limodzi ndi mitengo ya mkungudza ya ku Lebanoni. Mitengoyi ikunena kuti, ‘Kuyambira pamene unaphedwa,Palibenso munthu wodula mitengo amene anabwera kudzatidula.’