-
Yesaya 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Chifukwa cha iwe, Mandawo adzutsa akufa,
Adzutsa atsogoleri* onse opondereza apadziko lapansi.
Amachititsa mafumu onse a mitundu ya anthu kunyamuka pamipando yawo yachifumu.
-