Yesaya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Okuona adzakuyangʼana modabwa.Adzakuyangʼanitsitsa nʼkunena kuti,‘Kodi munthu amene ankagwedeza dziko lapansi uja ndi ameneyu,Amene ankachititsa kuti maufumu anjenjemere,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:16 Yesaya 1, ptsa. 185-187
16 Okuona adzakuyangʼana modabwa.Adzakuyangʼanitsitsa nʼkunena kuti,‘Kodi munthu amene ankagwedeza dziko lapansi uja ndi ameneyu,Amene ankachititsa kuti maufumu anjenjemere,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:16 Yesaya 1, ptsa. 185-187