Yesaya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene anachititsa dziko lapansi kukhala ngati chipululu,Nʼkugonjetsa mizinda yake,+Amene sanalole kuti akaidi ake azipita kwawo?’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:17 Yesaya 1, ptsa. 185-187
17 Amene anachititsa dziko lapansi kukhala ngati chipululu,Nʼkugonjetsa mizinda yake,+Amene sanalole kuti akaidi ake azipita kwawo?’+