Yesaya 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa mʼmanda,Ngati mphukira* imene anthu amanyansidwa nayo,Imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga,Amene amatsikira kumiyala yamʼdzenje,Ngati mtembo wopondedwapondedwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Yesaya 1, ptsa. 185-187
19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa mʼmanda,Ngati mphukira* imene anthu amanyansidwa nayo,Imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga,Amene amatsikira kumiyala yamʼdzenje,Ngati mtembo wopondedwapondedwa.