-
Yesaya 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Konzekerani kupha ana ake
Chifukwa cha zolakwa za makolo awo,
Kuti asakhalenso ndi mphamvu nʼkuyamba kulamulira dziko lapansi
Komanso kudzaza dzikoli ndi mizinda yawo.”
-