Yesaya 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ine ndidzawaukira,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ndipo mʼBabulo ndidzachotsamo dzina, anthu otsala, ana komanso mbadwa,”+ akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Yesaya 1, tsa. 188 Buku la Onse, ptsa. 27-29 Nsanja ya Olonda,5/15/1993, ptsa. 5-6
22 “Ine ndidzawaukira,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ndipo mʼBabulo ndidzachotsamo dzina, anthu otsala, ana komanso mbadwa,”+ akutero Yehova.