-
Yesaya 14:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira kuti:
“Zimene ndikufuna kuchita, zidzachitika mmene ndikufunira,
Ndipo zimene ndasankha, ndi zimene zidzachitike.
-