Yesaya 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ana oyamba kubadwa a anthu onyozeka adzadya nʼkukhutaNdipo anthu osauka adzagona motetezeka,Koma ndidzapha anthu ako* ndi njala,Ndipo amene adzatsale mwa iwe adzaphedwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:30 Yesaya 1, ptsa. 191-192
30 Ana oyamba kubadwa a anthu onyozeka adzadya nʼkukhutaNdipo anthu osauka adzagona motetezeka,Koma ndidzapha anthu ako* ndi njala,Ndipo amene adzatsale mwa iwe adzaphedwa.+