-
Yesaya 14:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Lira mofuula geti iwe! Lira mokweza mzinda iwe!
Nonsenu mudzataya mtima, inu anthu a ku Filisitiya!
Chifukwa utsi ukubwera kuchokera kumpoto,
Ndipo palibe msilikali amene akutsalira pa magulu ake ankhondo.”
-