Yesaya 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi iwo adzawayankha chiyani amithenga ochokera ku mtundu wina? Adzawayankha kuti, Yehova waika maziko a Ziyoni,+Ndipo anthu onyozeka pakati pa anthu ake adzathawira mmenemo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:32 Yesaya 1, ptsa. 191-192
32 Kodi iwo adzawayankha chiyani amithenga ochokera ku mtundu wina? Adzawayankha kuti, Yehova waika maziko a Ziyoni,+Ndipo anthu onyozeka pakati pa anthu ake adzathawira mmenemo.