-
Yesaya 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Madzi a ku Nimurimu aumiratu.
Msipu wobiriwira wauma,
Udzu watha ndipo palibenso chilichonse chobiriwira chimene chatsala.
-