Yesaya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa kulira kwake kwamveka mʼdziko lonse la Mowabu.+ Kulira kwake kofuula kwamveka mpaka ku Egilaimu.Kulira kwake kofuula kwamveka mpaka ku Beere-elimu.
8 Chifukwa kulira kwake kwamveka mʼdziko lonse la Mowabu.+ Kulira kwake kofuula kwamveka mpaka ku Egilaimu.Kulira kwake kofuula kwamveka mpaka ku Beere-elimu.