-
Yesaya 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 “Perekani malangizo, chitani zimene zagamulidwa.
Chititsani kuti masana, mthunzi wanu ukhale waukulu ndipo uchititse mdima ngati wa usiku.
Bisani anthu amene abalalitsidwa ndipo amene akuthawa musawapereke kwa adani awo.
-