Yesaya 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa mʼmunda wako wazipatso,Ndipo mʼminda ya mpesa simukumveka nyimbo zachisangalalo kapena kufuula.+ Oponda mphesa sakupondanso mphesa kuti apange vinyo,Chifukwa ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+
10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa mʼmunda wako wazipatso,Ndipo mʼminda ya mpesa simukumveka nyimbo zachisangalalo kapena kufuula.+ Oponda mphesa sakupondanso mphesa kuti apange vinyo,Chifukwa ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+