14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha zaka zitatu, mofanana ndi zaka za munthu waganyu, ulemerero wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse ndipo anthu amene adzatsale adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+