Yesaya 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko sadzakhalanso mzinda,Adzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:1 Yesaya 1, ptsa. 195-196
17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko sadzakhalanso mzinda,Adzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.+