Yesaya 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sadzayangʼana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayangʼanitsitsa zinthu zimene zala zake zinapanga, kaya ndi mizati yopatulika* kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:8 Yesaya 1, ptsa. 196-197
8 Iye sadzayangʼana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayangʼanitsitsa zinthu zimene zala zake zinapanga, kaya ndi mizati yopatulika* kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.