Yesaya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:13 Yesaya 1, ptsa. 197-198
13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.