-
Yesaya 18:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu nonse okhala padziko lapansi,
Zimene mukuona zidzakhala ngati chizindikiro chimene chaikidwa pamapiri,
Ndipo mudzamva phokoso lofanana ndi kulira kwa lipenga.
-