-
Yesaya 18:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa nthawi yokolola isanafike,
Mitengo ikamaliza kuchita maluwa ndipo mphesa zikamapsa,
Mphukira zidzadulidwa ndi chida chosadzira mitengo
Ndipo tiziyangoyango take tidzadulidwa nʼkuchotsedwa.
-