Yesaya 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limenelo padzakhala mizinda 5 mʼdziko la Iguputo yolankhula chilankhulo cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira kuti idzakhala yokhulupirika kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:18 Yesaya 1, tsa. 204
18 Pa tsiku limenelo padzakhala mizinda 5 mʼdziko la Iguputo yolankhula chilankhulo cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira kuti idzakhala yokhulupirika kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko.