Yesaya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anati: “Mtumiki wanga Yesaya wayenda maliseche ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:3 Yesaya 1, tsa. 212
3 Kenako Yehova anati: “Mtumiki wanga Yesaya wayenda maliseche ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya.+