-
Yesaya 21:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Chifukwa iwo athawa malupanga, athawa lupanga limene lasololedwa,
Athawa uta umene wakungidwa ndiponso zoopsya zimene zikuchitika kunkhondo.
-