Yesaya 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uwu ndi uthenga wokhudza Chigwa cha Masomphenya:*+ Kodi chachitika nʼchiyani kuti anthu ako onse akwere pamadenga? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:1 Yesaya 1, ptsa. 231-233
22 Uwu ndi uthenga wokhudza Chigwa cha Masomphenya:*+ Kodi chachitika nʼchiyani kuti anthu ako onse akwere pamadenga?