Yesaya 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti,Mzinda waphokoso komanso tauni yonyada. Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupangaKapena kufera kunkhondo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:2 Yesaya 1, ptsa. 233-234
2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti,Mzinda waphokoso komanso tauni yonyada. Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupangaKapena kufera kunkhondo.+