Yesaya 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Olamulira ako onse ankhanza athawira limodzi.+ Anagwidwa kuti akhale akaidi popanda kugwiritsa ntchito uta. Onse amene anapezeka anagwidwa kuti akhale akaidi,+Ngakhale kuti anathawira kutali. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:3 Yesaya 1, ptsa. 231, 234
3 Olamulira ako onse ankhanza athawira limodzi.+ Anagwidwa kuti akhale akaidi popanda kugwiritsa ntchito uta. Onse amene anapezeka anagwidwa kuti akhale akaidi,+Ngakhale kuti anathawira kutali.