Yesaya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu a ku Elamu+ atenga kachikwama koikamo miviNdipo akwera magaleta ankhondo ndi mahatchi,Anthu a ku Kiri+ achotsa chophimbira* chishango. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:6 Yesaya 1, tsa. 235
6 Anthu a ku Elamu+ atenga kachikwama koikamo miviNdipo akwera magaleta ankhondo ndi mahatchi,Anthu a ku Kiri+ achotsa chophimbira* chishango.