-
Yesaya 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mudzakumba dziwe pakati pa makoma awiri, losungiramo madzi a dziwe lakale. Koma simudzadalira Wolipanga Wamkulu ndipo simudzaganizira za amene analipanga kale kwambiri.
-